Luka 9:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pamenepo, onse anadabwa ndi mphamvu zodabwitsa+ za Mulungu. Tsopano onse adakali odabwa ndi zonse zimene anali kuchita, Yesu anauza ophunzira ake kuti:
43 Pamenepo, onse anadabwa ndi mphamvu zodabwitsa+ za Mulungu. Tsopano onse adakali odabwa ndi zonse zimene anali kuchita, Yesu anauza ophunzira ake kuti: