Mateyu 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kanjere kameneka ndi kakang’ono kwambiri mwa njere zonse, koma kakamera kamakula kwambiri kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo umakhala mtengo, moti mbalame zam’mlengalenga+ zimabwera kudzapeza malo okhala munthambi zake.”+ Maliko 4:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 koma akakafesa, kamamera ndi kukula kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo kamapanga nthambi zikuluzikulu,+ moti mbalame zam’mlengalenga+ zimatha kupeza malo okhala mumthunzi wake.”+
32 Kanjere kameneka ndi kakang’ono kwambiri mwa njere zonse, koma kakamera kamakula kwambiri kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo umakhala mtengo, moti mbalame zam’mlengalenga+ zimabwera kudzapeza malo okhala munthambi zake.”+
32 koma akakafesa, kamamera ndi kukula kuposa mbewu zonse zakudimba ndipo kamapanga nthambi zikuluzikulu,+ moti mbalame zam’mlengalenga+ zimatha kupeza malo okhala mumthunzi wake.”+