Mateyu 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Anawafotokozeranso fanizo lina kuti: “Ufumu wakumwamba uli ngati zofufumitsa,+ zimene mkazi wina anazitenga ndi kuzisakaniza ndi ufa wokwana mbale zitatu zazikulu zoyezera, ndipo mtanda wonsewo unafufuma.”
33 Anawafotokozeranso fanizo lina kuti: “Ufumu wakumwamba uli ngati zofufumitsa,+ zimene mkazi wina anazitenga ndi kuzisakaniza ndi ufa wokwana mbale zitatu zazikulu zoyezera, ndipo mtanda wonsewo unafufuma.”