Mateyu 9:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano Yesu anayamba ulendo woyendera mizinda ndi midzi yonse. Anali kuphunzitsa m’masunagoge awo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa matenda amtundu uliwonse ndi zofooka zilizonse.+ Maliko 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndithudi, iye anadabwa kuona kuti anthuwo analibe chikhulupiriro. Ndipo anazungulira m’midzi yapafupi akuphunzitsa.+
35 Tsopano Yesu anayamba ulendo woyendera mizinda ndi midzi yonse. Anali kuphunzitsa m’masunagoge awo, kulalikira uthenga wabwino wa ufumu ndi kuchiritsa matenda amtundu uliwonse ndi zofooka zilizonse.+
6 Ndithudi, iye anadabwa kuona kuti anthuwo analibe chikhulupiriro. Ndipo anazungulira m’midzi yapafupi akuphunzitsa.+