Yohane 7:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Mudzandifunafuna,+ koma simudzandipeza, ndipo kumene ndidzapiteko inu simudzatha kukafikako.”+ Aroma 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma ngakhale kuti Aisiraeli anali kutsatira lamulo la chilungamo, sanalipeze lamulolo.+ 1 Timoteyo 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Menya nkhondo yabwino yosunga chikhulupiriro.+ Gwira mwamphamvu moyo wosatha. Anakuitanira moyo umenewu ndipo unalengeza momveka bwino+ zinthu zokhudzana ndi moyo umenewu pamaso pa mboni zambiri.
12 Menya nkhondo yabwino yosunga chikhulupiriro.+ Gwira mwamphamvu moyo wosatha. Anakuitanira moyo umenewu ndipo unalengeza momveka bwino+ zinthu zokhudzana ndi moyo umenewu pamaso pa mboni zambiri.