Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 14:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Atamva izi, mmodzi wa alendo anzake anamuuza kuti: “Wodala ndi munthu wakudya chakudya mu ufumu wa Mulungu.”+

  • Luka 22:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pakuti ndikukuuzani, sindidzadyanso pasika kufikira zonse zimene pasikayu akuimira zitakwaniritsidwa mu ufumu wa Mulungu.”+

  • Machitidwe 2:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Pakuti lonjezoli+ laperekedwa kwa inu, kwa ana anu ndi kwa onse akutali,+ onse amene Yehova Mulungu wathu angawasankhe.”+

  • Chivumbulutso 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Iwo anali kuimba nyimbo yatsopano,+ yakuti: “Inu ndinu woyenera kutenga mpukutuwo ndi kumatula zidindo zake zomatira, chifukwa munaphedwa, ndipo ndi magazi anu,+ munagula+ anthu kuti atumikire Mulungu.+ Anthu ochokera mu fuko lililonse, chinenero chilichonse, mtundu uliwonse, ndi dziko lililonse.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena