Luka 7:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Tsopano Mfarisi wina anaumiriza Yesu kuti akadye naye. Choncho anapita kunyumba+ ya Mfarisiyo ndipo anamupatsa chakudya. Luka 11:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Atalankhula zimenezi, Mfarisi wina anam’pempha kuti akadye naye.+ Choncho iye anapitadi kukadya chakudya.
36 Tsopano Mfarisi wina anaumiriza Yesu kuti akadye naye. Choncho anapita kunyumba+ ya Mfarisiyo ndipo anamupatsa chakudya.
37 Atalankhula zimenezi, Mfarisi wina anam’pempha kuti akadye naye.+ Choncho iye anapitadi kukadya chakudya.