11 Koma iye anawayankha kuti: “Ndani wa inu amene atakhala ndi nkhosa imodzi, ndiyeno nkhosayo n’kugwera m’dzenje+ tsiku la sabata, sangaigwire ndi kuitulutsa?+
15 Koma Ambuye anamuyankha kuti: “Onyenga inu,+ kodi aliyense wa inu samasula ng’ombe yake kapena bulu wake m’khola pa sabata ndi kupita naye kukam’mwetsa madzi?+