Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chotero pitani m’misewu yotuluka mumzinda, ndipo aliyense amene mukam’peze, mukamuitanire phwando laukwatili.’+

  • Mateyu 28:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Choncho pitani mukaphunzitse anthu a mitundu yonse+ kuti akhale ophunzira anga.+ Muziwabatiza+ m’dzina la Atate,+ ndi la Mwana,+ ndi la mzimu woyera,+

  • Machitidwe 13:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Chotero Paulo ndi Baranaba analankhula molimba mtima kuti: “Kunali koyenera kuti inu mukhale oyamba kuuzidwa mawu a Mulungu.+ Koma popeza kuti mukuwatayira kumbali+ ndipo mukudziweruza nokha kukhala osayenera moyo wosatha, ifeyo tikutembenukira kwa anthu a mitundu ina.+

  • 1 Akorinto 1:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mukuona mmene anakuitanirani, abale, kuti si ambiri amene anthu amawaona kuti ndi anzeru+ omwe anaitanidwa,+ si ambiri amphamvu+ amene anaitanidwa, si ambiri a m’mabanja achifumu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena