2 Akorinto 5:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero ndife+ akazembe+ m’malo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife.+ Monga okhala m’malo mwa Khristu tikupempha kuti:+ “Gwirizananinso ndi Mulungu.”
20 Chotero ndife+ akazembe+ m’malo mwa Khristu,+ ngati kuti Mulungu akuchonderera anthu kudzera mwa ife.+ Monga okhala m’malo mwa Khristu tikupempha kuti:+ “Gwirizananinso ndi Mulungu.”