Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 33:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Munthu amene anauza bambo ndi mayi ake kuti, ‘Sindinawaone.’

      Ngakhale abale ake sanawavomereze,+

      Ndipo ana ake sanawadziwe.

      Pakuti anasunga mawu anu,+

      Ndipo anapitiriza kusunga pangano lanu.+

  • Mateyu 10:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Amene amakonda kwambiri bambo ake kapena mayi ake kuposa ine sali woyenera ine. Komanso amene amakonda kwambiri mwana wake wamwamuna kapena wamkazi kuposa ine sali woyenera ine.+

  • Luka 18:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Yesu anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Palibe amene wasiya nyumba, mkazi, abale, makolo kapena ana, chifukwa cha ufumu wa Mulungu+

  • Yohane 12:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena