Mateyu 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamenepo Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse ndi kukutsatirani, kodi tidzapeza chiyani?”+ Luka 9:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Yesu anamuuza kuti: “Aliyense wogwira pulawo+ koma n’kumayang’ana zinthu za m’mbuyo+ sayenera ufumu wa Mulungu.” Afilipi 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma zinthu zimene zinali zaphindu kwa ine, zimenezo ndaziona kukhala zopanda phindu chifukwa cha Khristu.+
27 Pamenepo Petulo ananena kuti: “Taonani! Ife tasiya zinthu zonse ndi kukutsatirani, kodi tidzapeza chiyani?”+
62 Yesu anamuuza kuti: “Aliyense wogwira pulawo+ koma n’kumayang’ana zinthu za m’mbuyo+ sayenera ufumu wa Mulungu.”
7 Koma zinthu zimene zinali zaphindu kwa ine, zimenezo ndaziona kukhala zopanda phindu chifukwa cha Khristu.+