Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 5:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Inu ndinu mchere+ wa dziko lapansi. Koma ngati mchere watha mphamvu, kodi mphamvu yake angaibwezeretse motani? Sungagwire ntchito iliyonse koma ungafunike kuutaya kunja+ kumene anthu akaupondaponda.

  • Maliko 9:50
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 50 Mchere ndi wabwino, koma mcherewo ukatha mphamvu, kodi mungaibwezeretse bwanji?+ Khalani ndi mchere+ mwa inu nokha, ndipo sungani mtendere+ pakati panu.”

  • Akolose 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nthawi zonse mawu anu azikhala achisomo,+ okoma ngati kuti mwawathira mchere,+ kuti mudziwe mmene mungayankhire+ wina aliyense.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena