Mateyu 13:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+ Maliko 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako anawonjezera mawu akuti: “Amene ali ndi makutu akumva, amve.”+ Chivumbulutso 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene ali ndi makutu amve zimene mzimu+ ukunena ku mipingo.’+
43 Pa nthawi imeneyo olungama adzawala+ kwambiri ngati dzuwa+ mu ufumu wa Atate wawo. Amene ali ndi makutu amve.+