Mateyu 26:64 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 64 Yesu anamuyankha+ kuti: “Mwanena nokha.+ Ndipo ndikukuuzani anthu inu kuti, kuyambira tsopano+ mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+ Mateyu 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+
64 Yesu anamuyankha+ kuti: “Mwanena nokha.+ Ndipo ndikukuuzani anthu inu kuti, kuyambira tsopano+ mudzaona Mwana wa munthu+ atakhala kudzanja lamanja+ lamphamvu. Mudzamuonanso akubwera pamitambo yakumwamba.”+
11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa, ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe mfumu ya Ayuda?”+ Yesu anayankha kuti: “Mukunena nokha.”+