Agalatiya 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma nonsenu ndinu ana+ a Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro chanu mwa Khristu Yesu.