Ekisodo 31:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+ Deuteronomo 4:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Tsopano chilamulo+ chimene Mose anaika pamaso pa ana a Isiraeli ndi ichi. Yohane 7:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mose anakupatsani Chilamulo,+ si choncho kodi? Komatu palibe ngakhale mmodzi wa inu amene amamvera Chilamulocho. Nanga n’chifukwa chiyani inu mukufuna kundipha?”+
18 Ndiyeno atamaliza kulankhula naye paphiri la Sinai, anapatsa Mose miyala iwiri yosema ya Umboni,+ miyala yolembedwapo mawu ndi chala cha Mulungu.+
19 Mose anakupatsani Chilamulo,+ si choncho kodi? Komatu palibe ngakhale mmodzi wa inu amene amamvera Chilamulocho. Nanga n’chifukwa chiyani inu mukufuna kundipha?”+