Luka 9:62 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 62 Yesu anamuuza kuti: “Aliyense wogwira pulawo+ koma n’kumayang’ana zinthu za m’mbuyo+ sayenera ufumu wa Mulungu.”
62 Yesu anamuuza kuti: “Aliyense wogwira pulawo+ koma n’kumayang’ana zinthu za m’mbuyo+ sayenera ufumu wa Mulungu.”