Luka 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Satana analowa mwa Yudasi, wotchedwa Isikariyoti, mmodzi wa ophunzira 12 aja.+ Yohane 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+
18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+