Mateyu 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mofanana ndi zimenezi, Yohane anabwera ndipo sanali kudya kapena kumwa.+ Koma anthu ankanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’ Maliko 3:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Ananena zimenezi chifukwa iwo anali kumunena kuti: “Ali ndi mzimu wonyansa.”+ Luka 7:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mofanana ndi zimenezi, Yohane M’batizi anabwera ndipo sadya chakudya kapena kumwa vinyo, koma inu mumanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’+
18 Mofanana ndi zimenezi, Yohane anabwera ndipo sanali kudya kapena kumwa.+ Koma anthu ankanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’
33 Mofanana ndi zimenezi, Yohane M’batizi anabwera ndipo sadya chakudya kapena kumwa vinyo, koma inu mumanena kuti, ‘Ali ndi chiwanda.’+