Mateyu 8:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Atafika kutsidya linalo, m’dera la Agadara,+ anakumana ndi amuna awiri ogwidwa ndi ziwanda+ akuchokera m’manda achikumbutso. Amunawa anali ochititsa mantha nthawi zonse moti panalibe aliyense woyesa dala kudutsa msewu umenewo. Yohane 5:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake
28 Atafika kutsidya linalo, m’dera la Agadara,+ anakumana ndi amuna awiri ogwidwa ndi ziwanda+ akuchokera m’manda achikumbutso. Amunawa anali ochititsa mantha nthawi zonse moti panalibe aliyense woyesa dala kudutsa msewu umenewo.
28 Musadabwe nazo zimenezi, chifukwa idzafika nthawi pamene onse ali m’manda achikumbutso+ adzamva mawu ake