Yohane 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano panali munthu wina amene anali kudwala, dzina lake Lazaro. Anali wa m’mudzi wa Betaniya, kwawo kwa Mariya ndi m’bale wake Marita.+ Yohane 11:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Atanena zimenezi, anafuula mokweza mawu kuti: “Lazaro, tuluka!”+
11 Tsopano panali munthu wina amene anali kudwala, dzina lake Lazaro. Anali wa m’mudzi wa Betaniya, kwawo kwa Mariya ndi m’bale wake Marita.+