Mateyu 21:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri Luka 19:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Atangofika pafupi ndi msewu wochokera m’phiri la Maolivi khamu lonse la ophunzirawo linayamba kukondwera ndi kutamanda Mulungu mokweza mawu chifukwa cha ntchito zamphamvu zimene anaona.+
15 Ansembe aakulu ndi alembi ataona zodabwitsa zimene anachitazo+ komanso anyamata amene anali kufuula m’kachisimo kuti: “M’pulumutseni+ Mwana wa Davide!”+ anakwiya kwambiri
37 Atangofika pafupi ndi msewu wochokera m’phiri la Maolivi khamu lonse la ophunzirawo linayamba kukondwera ndi kutamanda Mulungu mokweza mawu chifukwa cha ntchito zamphamvu zimene anaona.+