Yohane 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mulungunso payekha amulemekeza iye,+ ndipo amulemekeza nthawi yomwe ino. Yohane 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba+ ndi kunena kuti: “Atate, nthawi yafika, lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+
17 Yesu atalankhula zinthu zimenezi, anakweza maso ake kumwamba+ ndi kunena kuti: “Atate, nthawi yafika, lemekezani mwana wanu, kuti mwana wanu akulemekezeni.+