12 kuti kupenya azipenya ndithu, koma osaona, ndi kuti kumva azimva ndithu, koma osazindikira tanthauzo lake, kutinso asatembenuke ndi kukhululukidwa.”+
27 Pakuti anthu awa aumitsa mtima wawo, ndipo amva ndi makutu awo koma osalabadira. Iwo atseka maso awo, kuti asaone ndi maso awo, asamve ndi makutu awo ndi kuti asazindikire ndi mtima wawo n’kutembenuka kuti ine ndiwachiritse.”’+