Mateyu 10:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 “Amene wakulandirani walandiranso ine, ndipo amene walandira ine walandiranso amene anandituma.+ Mateyu 25:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma poyankha mfumuyo+ idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Pa mlingo umene munachitira zimenezo mmodzi wa abale+ anga aang’ono+ awa, munachitira ine amene.’+
40 Koma poyankha mfumuyo+ idzawauza kuti, ‘Ndithu ndikukuuzani, Pa mlingo umene munachitira zimenezo mmodzi wa abale+ anga aang’ono+ awa, munachitira ine amene.’+