Luka 6:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komanso anasankha Yudasi mwana wa Yakobo, ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anam’pereka.+ Machitidwe 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+
16 Komanso anasankha Yudasi mwana wa Yakobo, ndi Yudasi Isikariyoti, amene pambuyo pake anam’pereka.+
13 Atafika mumzindawo anakwera m’chipinda cham’mwamba,+ mmene anali kukhala. Mmenemo munali Petulo, Yohane, Yakobo, Andireya, Filipo, Tomasi, Batolomeyo, Mateyu, Yakobo mwana wa Alifeyo, Simoni wachangu uja komanso Yudasi mwana wa Yakobo.+