Maliko 4:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Chotero anawauza mawu mwa mafanizo ambiri+ oterewa, malinga ndi zimene akanakwanitsa kumva. 1 Akorinto 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero abale, sindinathe kulankhula nanu monga anthu auzimu,+ koma monga anthu oganiza ngati anthu a m’dzikoli,* monga tiana+ mwa Khristu.
3 Chotero abale, sindinathe kulankhula nanu monga anthu auzimu,+ koma monga anthu oganiza ngati anthu a m’dzikoli,* monga tiana+ mwa Khristu.