Mateyu 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musatilowetse m’mayesero,+ koma mutilanditse kwa woipayo.’+ 2 Atesalonika 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma Ambuye ndi wokhulupirika ndipo adzakulimbitsani ndi kukutetezani kwa woipitsitsayo.+ 1 Yohane 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tikudziwa kuti munthu aliyense amene ali mwana wa Mulungu+ sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, koma mwana*+ wa Mulungu amamuyang’anira, ndipo woipayo samugwira.+
18 Tikudziwa kuti munthu aliyense amene ali mwana wa Mulungu+ sakhala ndi chizolowezi chochita tchimo, koma mwana*+ wa Mulungu amamuyang’anira, ndipo woipayo samugwira.+