1 Atesalonika 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti Mulungu sanatiitane mwa kulekerera zodetsa, koma kuti tikhale oyera.+ Aheberi 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mwa “chifuniro”+ chimenecho, tayeretsedwa+ kudzera m’thupi la Yesu Khristu loperekedwa nsembe+ kamodzi+ kokha.
10 Mwa “chifuniro”+ chimenecho, tayeretsedwa+ kudzera m’thupi la Yesu Khristu loperekedwa nsembe+ kamodzi+ kokha.