Mateyu 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, pakuti mtsikanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola.+ Maliko 5:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Atalowa mkati, anafunsa anthuwo kuti: “N’chifukwa chiyani mukubuma ndi kulira motere? Mwana wamng’onoyu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Yohane 11:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yesu anati: “Kodi sindinakuuze kuti ngati ukhulupirira udzaona ulemerero wa Mulungu?”+ Machitidwe 9:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+
24 Yesu anawauza kuti: “Tulukani muno, pakuti mtsikanayu sanamwalire ayi, koma akugona.”+ Atanena zimenezi, anthuwo anayamba kum’seka monyodola.+
39 Atalowa mkati, anafunsa anthuwo kuti: “N’chifukwa chiyani mukubuma ndi kulira motere? Mwana wamng’onoyu sanamwalire ayi, koma akugona.”+
40 Koma Petulo anatulutsa anthu onse,+ ndiyeno anagwada pansi ndi kupemphera. Kenako anatembenukira mtembowo ndi kunena kuti: “Tabita, dzuka!” Pamenepo mayiyo anatsegula maso ake, ndipo mmene anaona Petulo, anadzuka n’kukhala tsonga.+