Machitidwe 5:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Ndipo tsiku ndi tsiku m’kachisi ndiponso kunyumba ndi nyumba,+ anapitiriza mwakhama kuphunzitsa+ ndi kulengeza uthenga wabwino wonena za Khristu, Yesu.+
42 Ndipo tsiku ndi tsiku m’kachisi ndiponso kunyumba ndi nyumba,+ anapitiriza mwakhama kuphunzitsa+ ndi kulengeza uthenga wabwino wonena za Khristu, Yesu.+