Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ine ndaima pamaso panu. Munditsutse pamaso pa Yehova ndi pamaso pa wodzozedwa+ wake: Alipo kodi amene ndinam’tengerapo ng’ombe kapena bulu wake?+ Alipo kodi amene ndinam’chitirapo chinyengo, kapena kum’pondereza? Kodi ndinalandirapo chiphuphu kwa aliyense kuti ndisaone zimene anachita?+ Ndili wokonzeka kukubwezerani anthu inu.”+

  • Mateyu 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chiritsani odwala,+ ukitsani anthu akufa, yeretsani akhate, tulutsani ziwanda. Munalandira kwaulere, patsani kwaulere.+

  • 1 Akorinto 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ngati anthu ena amagwiritsa ntchito ufulu umenewu pa inu,+ kodi ife sitili oyenera kutero kuposa amenewo? Ngakhale zili choncho, sitinagwiritse ntchito ufulu umenewo,+ koma timadzichitira tokha zinthu zonse, kuti tisapereke chododometsa chilichonse ku uthenga wabwino+ wonena za Khristu.

  • 2 Akorinto 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tipatseni malo m’mitima mwanu.+ Ifetu sitinalakwire aliyense, sitinaipitse aliyense, ndipo sitinachenjerere aliyense.+

  • Tito 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Pakuti woyang’anira ayenera kukhala wopanda chifukwa chomunenezera.+ Pokhala mtumiki*+ wa Mulungu, asakhale womva zake zokha,+ wa mtima wapachala,+ womwa mowa mwauchidakwa,*+ wandewu,+ kapena wokonda kupeza phindu mwachinyengo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena