Machitidwe 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atakhala kumeneko miyezi itatu, anaganiza zobwerera ku Makedoniya, chifukwa chakuti Ayuda anamukonzera chiwembu.+ Chiwembuchi anachikonza Paulo atangotsala pang’ono kuyamba ulendo wa pamadzi wopita ku Siriya.
3 Atakhala kumeneko miyezi itatu, anaganiza zobwerera ku Makedoniya, chifukwa chakuti Ayuda anamukonzera chiwembu.+ Chiwembuchi anachikonza Paulo atangotsala pang’ono kuyamba ulendo wa pamadzi wopita ku Siriya.