Machitidwe 21:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ali pafupi kutsiriza masiku 7,+ Ayuda ochokera ku Asia anaona Paulo ali m’kachisi. Chotero anayambitsa chisokonezo+ m’khamu lonse la anthu ndipo anamugwira.
27 Ali pafupi kutsiriza masiku 7,+ Ayuda ochokera ku Asia anaona Paulo ali m’kachisi. Chotero anayambitsa chisokonezo+ m’khamu lonse la anthu ndipo anamugwira.