Machitidwe 19:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kunena zoona, khamu lonse linali pa chipwirikiti, ena anali kufuula zina enanso zina.+ Mwakuti ambiri a iwo sanadziwe n’komwe chifukwa chimene anasonkhanira pamodzi.
32 Kunena zoona, khamu lonse linali pa chipwirikiti, ena anali kufuula zina enanso zina.+ Mwakuti ambiri a iwo sanadziwe n’komwe chifukwa chimene anasonkhanira pamodzi.