Machitidwe 21:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Atamulola, Paulo anaimirira pamasitepe ndi kukwezera anthuwo dzanja.+ Onse atakhala phee, analankhula nawo m’Chiheberi,+ kuti:
40 Atamulola, Paulo anaimirira pamasitepe ndi kukwezera anthuwo dzanja.+ Onse atakhala phee, analankhula nawo m’Chiheberi,+ kuti: