Machitidwe 26:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Komabe, dzuka ndi kuimirira.+ Pakuti ine ndaonekera kwa iwe kuti ndikusankhe kuti ukhale mtumiki ndi mboni+ ya zinthu zonse, zimene waona ndi zimene ndidzakuonetsa zokhudza ine.
16 Komabe, dzuka ndi kuimirira.+ Pakuti ine ndaonekera kwa iwe kuti ndikusankhe kuti ukhale mtumiki ndi mboni+ ya zinthu zonse, zimene waona ndi zimene ndidzakuonetsa zokhudza ine.