-
Machitidwe 9:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Nthawi yomweyo m’maso mwa Saulo munagwa tinthu tooneka ngati mamba a nsomba, ndipo anayambanso kuona. Kenako anapita kukabatizidwa,
-