Mateyu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chenjerani ndi anthu,+ pakuti adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani+ m’masunagoge awo.+
17 Chenjerani ndi anthu,+ pakuti adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani+ m’masunagoge awo.+