Mateyu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chenjerani ndi anthu,+ pakuti adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani+ m’masunagoge awo.+ Luka 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Koma zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani ndi kukuzunzani,+ adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakutengerani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+
17 Chenjerani ndi anthu,+ pakuti adzakuperekani kumakhoti aang’ono,+ ndipo adzakukwapulani+ m’masunagoge awo.+
12 “Koma zonsezi zisanachitike, anthu adzakugwirani ndi kukuzunzani,+ adzakuperekani kumasunagoge ndi kundende. Adzakutengerani kwa mafumu ndi abwanamkubwa chifukwa cha dzina langa.+