Mateyu 23:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 “Tsoka inu alembi ndi Afarisi, onyenga inu!+ Chifukwa mumafanana ndi manda opaka laimu,+ amene kunja kwake amaonekadi okongola, koma mkati mwake muli mafupa a anthu akufa ndi zonyansa zamitundu yonse.
27 “Tsoka inu alembi ndi Afarisi, onyenga inu!+ Chifukwa mumafanana ndi manda opaka laimu,+ amene kunja kwake amaonekadi okongola, koma mkati mwake muli mafupa a anthu akufa ndi zonyansa zamitundu yonse.