Machitidwe 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mwana wamwamuna wa mlongo wake wa Paulo anamva kuti anthuwo akonza zokamudikirira panjira,+ ndipo anapita ndi kukalowa kumpanda wa asilikali kukanena zimenezi kwa Paulo.
16 Koma mwana wamwamuna wa mlongo wake wa Paulo anamva kuti anthuwo akonza zokamudikirira panjira,+ ndipo anapita ndi kukalowa kumpanda wa asilikali kukanena zimenezi kwa Paulo.