Machitidwe 23:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma mwana wamwamuna wa mlongo wake wa Paulo anamva kuti anthuwo akonza zokamudikirira panjira,+ ndipo anapita ndi kukalowa kumpanda wa asilikali kukanena zimenezi kwa Paulo. Machitidwe 25:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndi kumupempha kuti awakomere mtima mwa kuitanitsa munthuyu kuti abwere ku Yerusalemu, kuti iwo amudikirire+ panjira ndi kumupha.
16 Koma mwana wamwamuna wa mlongo wake wa Paulo anamva kuti anthuwo akonza zokamudikirira panjira,+ ndipo anapita ndi kukalowa kumpanda wa asilikali kukanena zimenezi kwa Paulo.
3 ndi kumupempha kuti awakomere mtima mwa kuitanitsa munthuyu kuti abwere ku Yerusalemu, kuti iwo amudikirire+ panjira ndi kumupha.