Salimo 115:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yehova adzakuchulukitsani,+Inu ndi ana anu.+ 1 Akorinto 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotero wobzala+ kapena wothirira sali kanthu, koma Mulungu amene amakulitsa.+