Machitidwe 5:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezeka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+ Machitidwe 11:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Apanso, dzanja la Yehova+ linali nawo, ndipo ambiri amene anakhulupirira anatembenukira kwa Ambuye.+ Machitidwe 11:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Baranaba anali munthu wabwino, wodzazidwa ndi mzimu woyera komanso wachikhulupiriro. Ndipo khamu lalikulu ndithu linakhulupirira Ambuye.+
14 Komanso okhulupirira Ambuye anapitiriza kuwonjezeka, chifukwa amuna ndi akazi ambirimbiri anakhala ophunzira.+
21 Apanso, dzanja la Yehova+ linali nawo, ndipo ambiri amene anakhulupirira anatembenukira kwa Ambuye.+
24 Baranaba anali munthu wabwino, wodzazidwa ndi mzimu woyera komanso wachikhulupiriro. Ndipo khamu lalikulu ndithu linakhulupirira Ambuye.+