Machitidwe 21:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Paulo anatenga amunawo tsiku lotsatira ndi kukachita mwambo wa kudziyeretsa pamodzi ndi iwo.+ Kenako analowa m’kachisi, kukanena pamene masiku awo a mwambo wa kudziyeretsa adzathere,+ ndi pamene aliyense wa iwo adzamuperekere nsembe.+
26 Choncho Paulo anatenga amunawo tsiku lotsatira ndi kukachita mwambo wa kudziyeretsa pamodzi ndi iwo.+ Kenako analowa m’kachisi, kukanena pamene masiku awo a mwambo wa kudziyeretsa adzathere,+ ndi pamene aliyense wa iwo adzamuperekere nsembe.+