Machitidwe 23:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Paulo ataona kuti ena mwa iwo anali Asaduki+ ndipo ena anali Afarisi, anafuula m’khotimo kuti: “Amuna inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa+ chifukwa cha chiyembekezo cha kuuka+ kwa akufa.”
6 Tsopano Paulo ataona kuti ena mwa iwo anali Asaduki+ ndipo ena anali Afarisi, anafuula m’khotimo kuti: “Amuna inu, abale anga, ine ndine Mfarisi,+ mwana wa Afarisi. Pano ndikuweruzidwa+ chifukwa cha chiyembekezo cha kuuka+ kwa akufa.”