Luka 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ukatero udzakhala wodala, chifukwa alibe choti adzabweze kwa iwe. Pakuti udzabwezeredwa pa kuuka+ kwa anthu olungama.” Aheberi 11:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Akazi analandira akufa awo amene anauka kwa akufa.+ Koma anthu ena anazunzidwa chifukwa sanalole kusiya chikhulupiriro chawo kuti amasulidwe. Iwo anachita zimenezi kuti adzauke kwa akufa, komwe ndi kuuka kwabwino kwambiri.
14 Ukatero udzakhala wodala, chifukwa alibe choti adzabweze kwa iwe. Pakuti udzabwezeredwa pa kuuka+ kwa anthu olungama.”
35 Akazi analandira akufa awo amene anauka kwa akufa.+ Koma anthu ena anazunzidwa chifukwa sanalole kusiya chikhulupiriro chawo kuti amasulidwe. Iwo anachita zimenezi kuti adzauke kwa akufa, komwe ndi kuuka kwabwino kwambiri.