Agalatiya 5:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 kufatsa ndi kudziletsa.+ Palibe lamulo loletsa zinthu zoterezi.+ 2 Petulo 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 pa kudziwa zinthu kudziletsa, pa kudziletsa+ kupirira, pa kupirira kudzipereka kwa Mulungu,+